1 Mbiri 21:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kenako Yehova analamula mngelo+ uja kuti abwezere lupanga lake mʼchimake.