1 Mbiri 22:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma Yehova anandiuza kuti: ‘Iweyo wapha anthu* ambirimbiri ndipo wamenya nkhondo zikuluzikulu. Sudzamanga nyumba ya dzina langa,+ chifukwa wapha anthu ambirimbiri pamaso panga padziko lapansi.
8 Koma Yehova anandiuza kuti: ‘Iweyo wapha anthu* ambirimbiri ndipo wamenya nkhondo zikuluzikulu. Sudzamanga nyumba ya dzina langa,+ chifukwa wapha anthu ambirimbiri pamaso panga padziko lapansi.