1 Mbiri 22:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iyeyo ndi amene adzamange nyumba ya dzina langa.+ Adzakhala mwana wanga ndipo ine ndidzakhala bambo ake.+ Ndidzakhazikitsa mpando wake wachifumu mu Isiraeli ndipo udzakhalapo mpaka kalekale.’+
10 Iyeyo ndi amene adzamange nyumba ya dzina langa.+ Adzakhala mwana wanga ndipo ine ndidzakhala bambo ake.+ Ndidzakhazikitsa mpando wake wachifumu mu Isiraeli ndipo udzakhalapo mpaka kalekale.’+