1 Mbiri 22:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano mwana wanga, Yehova akhale nawe ndipo zinthu zikuyendere bwino. Umange nyumba ya Yehova Mulungu wako, mogwirizana ndi zimene iye analankhula zokhudza iweyo.+
11 Tsopano mwana wanga, Yehova akhale nawe ndipo zinthu zikuyendere bwino. Umange nyumba ya Yehova Mulungu wako, mogwirizana ndi zimene iye analankhula zokhudza iweyo.+