1 Mbiri 22:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Zinthu zidzakuyendera bwino ukamatsatira mosamala malamulo+ ndi ziweruzo zimene Yehova analamula Mose kuti apatse Aisiraeli.+ Khala wolimba mtima ndipo uchite zinthu mwamphamvu. Usaope kapena kuchita mantha.+
13 Zinthu zidzakuyendera bwino ukamatsatira mosamala malamulo+ ndi ziweruzo zimene Yehova analamula Mose kuti apatse Aisiraeli.+ Khala wolimba mtima ndipo uchite zinthu mwamphamvu. Usaope kapena kuchita mantha.+