1 Mbiri 22:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Palinso antchito ambirimbiri. Pali osema miyala, amisiri a miyala+ ndi a matabwa ndiponso akatswiri a ntchito zosiyanasiyana.+
15 Palinso antchito ambirimbiri. Pali osema miyala, amisiri a miyala+ ndi a matabwa ndiponso akatswiri a ntchito zosiyanasiyana.+