1 Mbiri 23:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Atatero, Alevi anawerengedwa kuyambira azaka 30 kupita mʼtsogolo.+ Anawerenga mwamuna aliyense mmodzi ndi mmodzi* ndipo onse anakwana 38,000.
3 Atatero, Alevi anawerengedwa kuyambira azaka 30 kupita mʼtsogolo.+ Anawerenga mwamuna aliyense mmodzi ndi mmodzi* ndipo onse anakwana 38,000.