1 Mbiri 23:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pa anthu amenewa, 24,000 anali oyangʼanira ntchito yapanyumba ya Yehova. Akapitawo ndi oweruza analipo 6,000.+
4 Pa anthu amenewa, 24,000 anali oyangʼanira ntchito yapanyumba ya Yehova. Akapitawo ndi oweruza analipo 6,000.+