1 Mbiri 23:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Panalinso alonda 4,000 apageti+ ndi anthu 4,000 otamanda+ Yehova poimba ndi zoimbira zimene Davide anati, “Zimenezi ndazipanga kuti tizitamandira Mulungu.”
5 Panalinso alonda 4,000 apageti+ ndi anthu 4,000 otamanda+ Yehova poimba ndi zoimbira zimene Davide anati, “Zimenezi ndazipanga kuti tizitamandira Mulungu.”