1 Mbiri 23:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Davide anawagawa mʼmagulu+ mogwirizana ndi ana a Levi: Gerisoni, Kohati ndi Merari.+