-
1 Mbiri 23:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Yahati anali mtsogoleri wawo ndipo wachiwiri wake anali Ziza. Koma Yeusi ndi Beriya analibe ana ambiri aamuna, choncho anawawerenga ngati nyumba imodzi ya makolo ndipo udindo wawo unali umodzi.
-