1 Mbiri 23:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ana a Amuramu anali Aroni+ ndi Mose.+ Koma Aroni anasankhidwa+ kuti iye ndi ana ake azitumikira mʼMalo Oyera Koposa mpaka kalekale. Komanso kuti azipereka nsembe pamaso pa Yehova, kumutumikira ndi kudalitsa anthu mʼdzina lake nthawi zonse.+
13 Ana a Amuramu anali Aroni+ ndi Mose.+ Koma Aroni anasankhidwa+ kuti iye ndi ana ake azitumikira mʼMalo Oyera Koposa mpaka kalekale. Komanso kuti azipereka nsembe pamaso pa Yehova, kumutumikira ndi kudalitsa anthu mʼdzina lake nthawi zonse.+