-
1 Mbiri 23:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Eliezara anamwalira koma analibe ana aamuna, anali ndi aakazi okhaokha. Choncho abale awo, ana a Kisi, anawatenga kukhala akazi awo.
-