-
1 Mbiri 23:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Amenewa anali ana a Levi potsatira nyumba za makolo awo ndiponso atsogoleri a nyumba za makolo awo. Iwo analembedwa komanso kuwerengedwa potsatira mndandanda wa mayina awo. Amenewa ankatumikira panyumba ya Yehova kuyambira azaka 20 kupita mʼtsogolo.
-