1 Mbiri 23:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ankathandizanso ntchito zokhudza mkate wosanjikiza,*+ ufa wosalala wa nsembe yambewu, mikate yopyapyala yopanda zofufumitsa,+ makeke ophika mʼchiwaya, ufa wokandakanda wosakaniza ndi mafuta+ ndiponso miyezo yosiyanasiyana.
29 Ankathandizanso ntchito zokhudza mkate wosanjikiza,*+ ufa wosalala wa nsembe yambewu, mikate yopyapyala yopanda zofufumitsa,+ makeke ophika mʼchiwaya, ufa wokandakanda wosakaniza ndi mafuta+ ndiponso miyezo yosiyanasiyana.