1 Mbiri 23:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Mʼmawa uliwonse ankaimirira+ kuti athokoze ndi kutamanda Yehova. Madzulo ankachitanso zimenezi.+