-
1 Mbiri 24:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Koma chifukwa chakuti ana a Eliezara anali ndi atsogoleri ambiri kuposa ana a Itamara, anawagawa mogwirizana ndi chiwerengero chawo. Ana a Eliezara anali ndi atsogoleri 16 a nyumba za makolo awo ndipo ana a Itamara anali ndi atsogoleri 8 a nyumba za makolo awo.
-