1 Mbiri 24:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pogawapo, anachita maere+ pakati pa magulu awiriwa chifukwa panali atsogoleri apamalo oyera ndi atsogoleri otumikira Mulungu woona ochokera mbali zonse ziwiri, kwa ana a Eliezara ndiponso kwa ana a Itamara.
5 Pogawapo, anachita maere+ pakati pa magulu awiriwa chifukwa panali atsogoleri apamalo oyera ndi atsogoleri otumikira Mulungu woona ochokera mbali zonse ziwiri, kwa ana a Eliezara ndiponso kwa ana a Itamara.