-
1 Mbiri 25:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Pa ana a Asafu, anatengapo Zakuri, Yosefe, Netaniya ndi Asarela. Ana akewa ankatsogoleredwa ndi Asafuyo, amenenso ankalosera, ndipo ankayangʼaniridwa ndi mfumu.
-