1 Mbiri 25:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kwa Yedutuni,+ anatengako ana ake awa: Gedaliya, Zeri, Yesaiya, Simeyi, Hasabiya ndi Matitiya,+ onse pamodzi analipo 6. Iwowa ankayangʼaniridwa ndi Yedutuni bambo awo, amene ankalosera ndi zeze ndipo ankayamika ndi kutamanda Yehova.+
3 Kwa Yedutuni,+ anatengako ana ake awa: Gedaliya, Zeri, Yesaiya, Simeyi, Hasabiya ndi Matitiya,+ onse pamodzi analipo 6. Iwowa ankayangʼaniridwa ndi Yedutuni bambo awo, amene ankalosera ndi zeze ndipo ankayamika ndi kutamanda Yehova.+