1 Mbiri 25:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Onsewa anali ana a Hemani, wamasomphenya wa mfumu pa zinthu za Mulungu woona pofuna kutamanda Mulungu.* Choncho Mulungu woona anapatsa Hemani ana aamuna 14 ndi ana aakazi atatu.
5 Onsewa anali ana a Hemani, wamasomphenya wa mfumu pa zinthu za Mulungu woona pofuna kutamanda Mulungu.* Choncho Mulungu woona anapatsa Hemani ana aamuna 14 ndi ana aakazi atatu.