1 Mbiri 25:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ana onsewa ankayangʼaniridwa ndi bambo awo poimba nyimbo panyumba ya Yehova. Ankaimba nyimbozo ndi zinganga, zoimbira za zingwe ndi azeze,+ potumikira panyumba ya Mulungu woona. Koma Asafu, Yedutuni ndi Hemani ankayangʼaniridwa ndi mfumu.
6 Ana onsewa ankayangʼaniridwa ndi bambo awo poimba nyimbo panyumba ya Yehova. Ankaimba nyimbozo ndi zinganga, zoimbira za zingwe ndi azeze,+ potumikira panyumba ya Mulungu woona. Koma Asafu, Yedutuni ndi Hemani ankayangʼaniridwa ndi mfumu.