1 Mbiri 25:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako anachita maere+ powagawira ntchito yoti azichita. Pochita maerewo, sankayangʼana kuti uyu ndi wamngʼono kapena wamkulu, katswiri kapena wophunzira kumene.
8 Kenako anachita maere+ powagawira ntchito yoti azichita. Pochita maerewo, sankayangʼana kuti uyu ndi wamngʼono kapena wamkulu, katswiri kapena wophunzira kumene.