-
1 Mbiri 26:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Hosa, mbadwa ya Merari anali ndi ana ndipo Simuri anali mtsogoleri wawo. Ngakhale kuti sanali woyamba kubadwa, bambo ake anamusankha kuti akhale mtsogoleri.
-