1 Mbiri 26:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho anachita maere+ ofanana kwa wamngʼono ndi wamkulu potsatira nyumba za makolo awo, kuti apeze ogwira ntchito pageti lililonse.
13 Choncho anachita maere+ ofanana kwa wamngʼono ndi wamkulu potsatira nyumba za makolo awo, kuti apeze ogwira ntchito pageti lililonse.