1 Mbiri 26:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Maere a Supimu ndi a Hosa+ anagwera kumadzulo pafupi ndi Geti la Saleketi, pamsewu wopita kumtunda. Gulu limodzi la alonda linakhala moyandikana ndi gulu lina la alonda.
16 Maere a Supimu ndi a Hosa+ anagwera kumadzulo pafupi ndi Geti la Saleketi, pamsewu wopita kumtunda. Gulu limodzi la alonda linakhala moyandikana ndi gulu lina la alonda.