1 Mbiri 26:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kumbali ya Alevi, Ahiya ankayangʼanira chuma chamʼnyumba ya Mulungu woona ndiponso zinthu zimene anaziyeretsa kuti zikhale zopatulika.*+
20 Kumbali ya Alevi, Ahiya ankayangʼanira chuma chamʼnyumba ya Mulungu woona ndiponso zinthu zimene anaziyeretsa kuti zikhale zopatulika.*+