1 Mbiri 26:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pa ana a Ladani, panali Yehieli.+ Ana amenewo anali mbadwa za Gerisoni kudzera mwa Ladani ndipo anali atsogoleri a nyumba za makolo za Ladani mbadwa ya Gerisoni
21 Pa ana a Ladani, panali Yehieli.+ Ana amenewo anali mbadwa za Gerisoni kudzera mwa Ladani ndipo anali atsogoleri a nyumba za makolo za Ladani mbadwa ya Gerisoni