1 Mbiri 26:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Anayeretsa zinthu zimene anazitenga+ kunkhondo+ kuti azizigwiritsa ntchito panyumba ya Yehova.