1 Mbiri 27:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Woyangʼanira wa gulu la mwezi wachiwiri anali Dodai+ wa ku Ahohi+ ndipo Mikiloti anali mtsogoleri. Gulu lake linali ndi anthu 24,000.
4 Woyangʼanira wa gulu la mwezi wachiwiri anali Dodai+ wa ku Ahohi+ ndipo Mikiloti anali mtsogoleri. Gulu lake linali ndi anthu 24,000.