1 Mbiri 27:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mtsogoleri wa 4, wa mwezi wa 4, anali Asaheli+ mchimwene wake wa Yowabu+ ndipo mwana wake Zebadiya analowa mʼmalo mwake. Gulu lake linali ndi anthu 24,000.
7 Mtsogoleri wa 4, wa mwezi wa 4, anali Asaheli+ mchimwene wake wa Yowabu+ ndipo mwana wake Zebadiya analowa mʼmalo mwake. Gulu lake linali ndi anthu 24,000.