1 Mbiri 27:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mtsogoleri wa 11, wa mwezi wa 11, anali Benaya+ wa ku Piratoni, wa fuko la Efuraimu. Gulu lake linali ndi anthu 24,000.
14 Mtsogoleri wa 11, wa mwezi wa 11, anali Benaya+ wa ku Piratoni, wa fuko la Efuraimu. Gulu lake linali ndi anthu 24,000.