1 Mbiri 28:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndipo pa ana anga onse (poti Yehova wandipatsa ana ambiri)+ anasankha mwana wanga Solomo+ kuti akhale pampando wachifumu wa ufumu wa Yehova, kuti alamulire Isiraeli.+
5 Ndipo pa ana anga onse (poti Yehova wandipatsa ana ambiri)+ anasankha mwana wanga Solomo+ kuti akhale pampando wachifumu wa ufumu wa Yehova, kuti alamulire Isiraeli.+