1 Mbiri 28:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anandiuza kuti: ‘Mwana wako Solomo ndi amene adzamange nyumba yanga ndiponso mabwalo anga, chifukwa ndamusankha kuti akhale mwana wanga ndipo ine ndidzakhala bambo ake.+
6 Anandiuza kuti: ‘Mwana wako Solomo ndi amene adzamange nyumba yanga ndiponso mabwalo anga, chifukwa ndamusankha kuti akhale mwana wanga ndipo ine ndidzakhala bambo ake.+