1 Mbiri 28:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Akamatsatira malamulo anga ndi ziweruzo zanga+ ndi mtima wonse ngati mmene akuchitira panopa, ndidzakhazikitsa ufumu wake ndipo udzakhalapo mpaka kalekale.’+
7 Akamatsatira malamulo anga ndi ziweruzo zanga+ ndi mtima wonse ngati mmene akuchitira panopa, ndidzakhazikitsa ufumu wake ndipo udzakhalapo mpaka kalekale.’+