-
1 Mbiri 28:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Tsopano ndikulankhula pamaso pa Aisiraeli onse, amene ndi mpingo wa Yehova, ndiponso Mulungu wathu akumva zimenezi: Muzifufuza ndi kutsatira mosamala malamulo onse a Yehova Mulungu wanu, kuti dziko labwinoli likhale lanu+ ndi kuti mudzasiyire ana anu obwera pambuyo panu monga cholowa chawo mpaka kalekale.
-