1 Mbiri 28:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Komanso anamʼpatsa malangizo okhudza magulu a ansembe+ ndi a Alevi, ntchito yonse yokhudza utumiki wapanyumba ya Yehova ndiponso malangizo okhudza ziwiya zonse za utumiki wapanyumba ya Yehova.
13 Komanso anamʼpatsa malangizo okhudza magulu a ansembe+ ndi a Alevi, ntchito yonse yokhudza utumiki wapanyumba ya Yehova ndiponso malangizo okhudza ziwiya zonse za utumiki wapanyumba ya Yehova.