15 kulemera kwa zoikapo nyale zagolide+ ndi nyale zake zagolide, kulemera kwa zoikapo nyale zosiyanasiyana ndi nyale zake, kulemera kwa zoikapo nyale zasiliva komanso kulemera kwa choikapo nyale chilichonse ndi nyale zake mogwirizana ndi ntchito zake;