1 Mbiri 28:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Anamuuzanso za kulemera kwa golide woyengedwa bwino wa guwa lansembe la zofukiza+ ndiponso golide wa chifaniziro cha galeta,+ kutanthauza akerubi+ agolide otambasula mapiko awo kuphimba likasa la pangano la Yehova.
18 Anamuuzanso za kulemera kwa golide woyengedwa bwino wa guwa lansembe la zofukiza+ ndiponso golide wa chifaniziro cha galeta,+ kutanthauza akerubi+ agolide otambasula mapiko awo kuphimba likasa la pangano la Yehova.