1 Mbiri 29:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 golide wodzapangira zinthu zagolide, siliva wodzapangira zinthu zasiliva ndi siliva woti amisiri adzagwiritse ntchito. Tsopano ndani lero wakonzeka kupereka mphatso kwa Yehova?”+ 1 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 29:5 Nsanja ya Olonda,7/1/1990, tsa. 31
5 golide wodzapangira zinthu zagolide, siliva wodzapangira zinthu zasiliva ndi siliva woti amisiri adzagwiritse ntchito. Tsopano ndani lero wakonzeka kupereka mphatso kwa Yehova?”+