1 Mbiri 29:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho akalonga a nyumba za makolo, akalonga a mafuko a Aisiraeli, atsogoleri a magulu a anthu 1,000 ndi a magulu a anthu 100+ ndiponso atsogoleri oyangʼanira ntchito za mfumu,+ anabwera nʼkuyamba kupereka zinthu mwa kufuna kwawo.
6 Choncho akalonga a nyumba za makolo, akalonga a mafuko a Aisiraeli, atsogoleri a magulu a anthu 1,000 ndi a magulu a anthu 100+ ndiponso atsogoleri oyangʼanira ntchito za mfumu,+ anabwera nʼkuyamba kupereka zinthu mwa kufuna kwawo.