1 Mbiri 29:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iwo anapereka golide wokwana matalente 5,000, madariki* 10,000, siliva wokwana matalente 10,000, kopa wokwana matalente 18,000 ndi zitsulo zokwana matalente 100,000. Anapereka zonsezi kuti zigwire ntchito panyumba ya Mulungu woona. 1 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 29:7 Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), ptsa. 2141-2142, 2242 Nsanja ya Olonda,8/1/2009, tsa. 30
7 Iwo anapereka golide wokwana matalente 5,000, madariki* 10,000, siliva wokwana matalente 10,000, kopa wokwana matalente 18,000 ndi zitsulo zokwana matalente 100,000. Anapereka zonsezi kuti zigwire ntchito panyumba ya Mulungu woona.