1 Mbiri 29:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Munthu aliyense amene anali ndi miyala yamtengo wapatali anaipereka ku chuma chapanyumba ya Yehova, chomwe Yehiela+ mbadwa ya Gerisoni+ ankayangʼanira.
8 Munthu aliyense amene anali ndi miyala yamtengo wapatali anaipereka ku chuma chapanyumba ya Yehova, chomwe Yehiela+ mbadwa ya Gerisoni+ ankayangʼanira.