1 Mbiri 29:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Anthuwo anasangalala chifukwa cha nsembe zaufulu zimene anapereka, chifukwa anapereka nsembezo kwa Yehova ndi mtima wonse.+ Nayenso Mfumu Davide anasangalala kwambiri.
9 Anthuwo anasangalala chifukwa cha nsembe zaufulu zimene anapereka, chifukwa anapereka nsembezo kwa Yehova ndi mtima wonse.+ Nayenso Mfumu Davide anasangalala kwambiri.