-
1 Mbiri 29:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Kenako Davide anauza mpingo wonse kuti: “Tsopano tamandani Yehova Mulungu wanu!” Choncho anthu onsewo anayamba kutamanda Yehova Mulungu wa makolo awo ndipo anagwadira Yehova ndi mfumu nʼkuwerama mpaka nkhope zawo kufika pansi.
-