1 Mbiri 29:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Nthawi yonse imene iye analamulira Isiraeli inali zaka 40. Ku Heburoni analamulira zaka 7+ ndipo ku Yerusalemu analamulira zaka 33.+
27 Nthawi yonse imene iye analamulira Isiraeli inali zaka 40. Ku Heburoni analamulira zaka 7+ ndipo ku Yerusalemu analamulira zaka 33.+