1 Mbiri 29:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kenako iye anamwalira ali wokalamba,+ atakhala ndi moyo wautali, chuma ndiponso ulemerero. Ndiyeno mwana wake Solomo anakhala mfumu mʼmalo mwake.+
28 Kenako iye anamwalira ali wokalamba,+ atakhala ndi moyo wautali, chuma ndiponso ulemerero. Ndiyeno mwana wake Solomo anakhala mfumu mʼmalo mwake.+