-
1 Mbiri 29:30Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
30 Analembanso nkhani zonse zokhudza ufumu wake, mphamvu zake, zinthu zimene zinachitika pa moyo wake ndiponso zomwe zinachitikira Aisiraeli onse ndi maufumu onse owazungulira.
-