2 Mbiri 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Ufumu wa Solomo mwana wa Davide unakhala wamphamvu. Yehova Mulungu wake anali naye ndipo anamuchititsa kukhala wamphamvu kwambiri.+
1 Ufumu wa Solomo mwana wa Davide unakhala wamphamvu. Yehova Mulungu wake anali naye ndipo anamuchititsa kukhala wamphamvu kwambiri.+