-
2 Mbiri 1:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Solomo anaitanitsa Aisiraeli onse, atsogoleri a magulu a anthu 1,000, atsogoleri a magulu a anthu 100, oweruza ndi akuluakulu onse a mu Isiraeli, amene anali atsogoleri a nyumba za makolo awo.
-